Achinyama enanso 140 wapsa wa ku Israel: Katswiri akhuzidwa akuti boma likuchulusa chinsinsi

Achinyamata okwana 140 akuyembekezeka kunyamuka mdziko muno lachitatu kupita ku Israel komwe azikagwira ntchito ku minda. Koma olankhulapo pa nkhani za ufulu,  a Michael Kayiyatsa ati pomwe ndondomekoyi ndi yabwino, boma likuyenera kumachita machawi kufotokozera anthu momwe ntchito yotumiza achinyamata ku Israel ikuyendera kuopa manong’onong’o. Ngakhale zili choncho, aJustice Kangulu omwe ndi mkulu wa kampani […]

The post Achinyama enanso 140 wapsa wa ku Israel: Katswiri akhuzidwa akuti boma likuchulusa chinsinsi appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください