Achibale afukula manda a m’bale wawo ku Machinjiri

Kunali chipwilikiti kwa Jumbe ku Makhetha mdera la Machinjiri mumzinda wa Blantyre pomwe anthu Lolemba anafukula manda a m’bale wawo poganizira kuti anthu ena anaba bokosi lomwe anamuikamo. Nkhaniyi ikutsatira mphekesera zomwe zakhala zikuveka kudelari kuti anthu ena achipongwe anafukula ndikuba bokosi la malemu Olive Balakasi omwe anamwalira kumayambiliro achaka chino ndipo thupi lawo lina […]

The post Achibale afukula manda a m’bale wawo ku Machinjiri appeared first on Malawi24.

close

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

Generated by Feedzy