Achewa akwiya ndi ulaliki wa m’busa Yasin Gama

Wolemba: Gracious  Zinazi Lilongwe District Council kudzera mwa bwanankubwa wake Dr Lawford Palani, yaitanitsa msonkhano okhudza nkhani ya ulaliki wa m’busa Hamilton Yasin Gama yemwe wakwiyitsa anthu a mtundu wa Chewa chifukwa chowanyazitsira chikhalidwe chawo. Ku msonkhanowu aitanitsa Kalembera wankulu wa C.C.A.P Nkhoma Synod, a Chewa Heritage, Chairperson wa Chiefs Forum mu boma la Lilongwe, […]

The post Achewa akwiya ndi ulaliki wa m’busa Yasin Gama appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です