Oyimba nyimbo za hipapu Ace Jizzy komaso Bee Jay, akana K12 miliyoni yomwe malume awo anati awapatsa ngati awiriwa angavomere kusiya kuyimba nyimbo za chikunja ndikuyamba kuyimba nyimbo zauzimu. Malume a anyamatawa a Israel Ndelezina omwe ndi mtumiki wa Mulungu, analemba patsamba lawo la nchezo la fesibuku kufotokoza za khumbo lawo loti Ace Jizzy komaso […]
The post Ace Jizzy, Bee Jay akana K12m kuti ayambe kuyiba nyimbo zauzimu appeared first on Malawi24.
Moni Malawi 