Bungwe lothana ndi katangale la Anti-Corruption Bureau lakhazikitsa bukhu la tsopano lotchedwa “Anti-Corruption Source Book” lomwe lidzigwilisidwa ntchito ndi aphunzitsi a kupulaimale. Bukhuli lomwe alikhazikitsa dzulo ku Lilongwe cholinga chake ndi kuphunzitsa chikhalidwe, umunthu komanso mzimu wa kulimbikira pakati pa ana m’dziko muno. Oyang’anila ntchito ku bungweli a Martha Chizuma, anati, bukhuli lithandiza kubwelesa m’bado […]
The post ACB yakhazikitsa bukhu appeared first on Malawi 24.