Abambo atatu ali m’manja mwa apolisi mu mzinda wa Lilongwe powaganizira kuti adapha ndi kukwilira mwa chinsinsi mulamu wawo a Luciano Masiye a zaka 26. Malingana ndi mneneli wa Polisi ya Lilongwe a Hastings Chigalu, izi zidachitika m’mudzi mwa Lumwila m’bomali, ndipo a Chigalu atsimikiza kuti atatuwa ndi a Polofesa Posiyano a zaka 24, a […]
The post Abambo atatu anjatidwa kamba kopha mulamu wawo appeared first on Malawi 24.