Abambo anayi amangidwa powaganizila kuti anapha mnyamata wa zaka 18

Apolisi m’boma la Balaka amanga abambo anayi powaganizira kuti ndiwo adachitira chiwembu komanso kupha ophunzira wa pa sukulu ya sekondale ya St.Charles Lwangwa Gift Libuda. Ophunzirayu yemwe adali ndi zaka 18 zakubadwa adachitilidwa chiwembu pa 11 September, Chaka chomwechino pomwe adakwera galimoto la mtundu wa Toyota Sienta pa ulendo wake ochokera kwa Chiendausiku kupita ku […]

The post Abambo anayi amangidwa powaganizila kuti anapha mnyamata wa zaka 18 appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください