Bungwe lotsogolera ntchito yolimbana ndi matenda a Edzi la National Aids Commission (NAC), lati kafukufuku akuonetsa kuti a bambo ambiri akumangodziyendera osayezetsa magazi pomwe akuti atsikana a chichepere makamaka m’sukulu zaukachenjede ndi omwe akutenga kwambiri kachiromboka kamba ka “ma blesser”. Izi ndi malingana ndi mkulu owona zopewa kachirombo ka HIV ku bungwe la NAC a […]
The post Abambo ambiri sanayezetse magazi, atsikana achichepere akutenga HIV kwambiri – yatelo NAC appeared first on Malawi 24.