Mkulu oyang’anila zaumoyo m’boma la Chiradzulu Dr. Jamson Chausa wadandaula ndikuchepekedwa komwe kukhalepo pamene bungwe la Medicines San Frontiers (MSF) ikhale ikuchoka bomali. Izi amayakhula pa mwambo osazikana ndi mafumu komanso ma khansala ndi adindo ena omwe MSF inakoza dzulo ku ma ofesi awo ku Chiradzulu. Mwa zina iwo anati MSF yakhala ikuthandiza kwambiri kwa […]
The post A zaumoyo adandaula ndi kuchoka kwa MSF ku Chiradzulu appeared first on Malawi 24.