Nthambi yoona zanyengo ndi kusintha kwa nyengo m’dziko lino lachenjeza a Malawi maka akuchigawo chakum’mwera ponena kuti lero pa 14 December 2023, mvula yamphamvu ikhale ikugwa. Malingana ndi uthenga omwe watulutsa ndi mneneli wa nthambiyi, a Yobu Kachiwanda ati mvula ya mphepo ndi yamkuntho ikuyembekezereka kugwa maka mchigawo chakum’mwera ndipo ati kotero nkofunika kuti anthu […]
The post A zanyengo apempha a Malawi kuti akhale osamala pamene mvula ya mphamvu ikhale ikugwa appeared first on Malawi 24.