Patangodutsa ma sabata ochepa chipani Cha Democratic Progressive Party DPP chitachotsa kamanso kuimika ena mwa ma Membala ake omwe m’modzi mwa iwo ndi a Uladi Mussa, iwo tsopano ati alowa chipani cha Malawi Congress ponena kuti iwo akana chibwana Cha ku DPP. A Mussa awonetsedwa ku guru ndi wachiwiri kwa mulembi wa chipani cha MCP […]
The post A Uladi Mussa alowa MCP: Ati “Fotseki DPP” appeared first on Malawi 24.