Bungwe la HRDC lati vuto la kusowa kwa mafuta lomwe dziko lino likukumana nalo, ndi chizindikiro kuti boma lalephera. Mu chikalata chomwe chasainidwa ndi wapampando wa bungweli a Gift Trapence, vuto la mafutali silinakhudze Amalawi okha koma lakhudzanso chuma cha dziko lino chomwe chili kalenso pa mavuto a dzaoneni. HRDC yati kulephera kwa boma kukonza […]
The post A Trapence a HRDC ikuti kusowa kwa kwa mafuta nchizindikiro kuti boma lalephera appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.