Apolisi ku Lilongwe anamenya kumsana kwa oyimba Jetu, watero mmayi wazamalonda Dorothy Shonga yemwe amadziwika kwambiri kuti Cash Madam. Izi zinatsatira kusamvana komwe kunabuka pomwe apolisi ndi ena aku nthambi yotelera msonkho ya MRA paza zikalata za galimoto ya Dorothy yomwe anthuwa amayendera. Malingana ndi Shonga yemwe wati chipwilikitichi chinadza kuyambila malo achipikisheni a Nathenje […]
The post A Polisi ku Nathenje amenya woyimba wokalamba Jetu kunsana, watero Dorothy Shonga appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.