A polisi m’boma la Machinga alimbikitsa chitetezo pakati pamalire a dziko la Malawi ndi Mozambique pomwe akhazikitsa makomiti owona zachitetezo chakumadera akumidzi. A Polisiwa alangizanso mzika za dziko lino kuti zidzikhala tcheru pankhani za umbanda ndi umbava komanso adzikanena ku polisi ngati akuwona anthu okayikitsa mdera lawo. Mkulu woona zachitetedzo chakumadera akumidzi pa polisi ya […]
The post A Polisi Boma la Machinga alimbikitsa chitetezo m’malire a Malawi ndi Mozambique appeared first on Malawi 24.