A polisi awiri amangidwa ku Karonga pothandizira kulowesa mowa mu cell

Apolisi amanga a polisi anzawo awiri, omwe amagwira ntchito ku polisi ya Karonga, powaganizira kuti akukhudzidwa ndi nkhani yolowetsa mowa komanso lamya za mmanja mu chitokosi cha apolisi m’bomali. Kumangidwa kwa apolisiwa kukudza pomwe kanema ina inafala pa masamba a mchezo imene imaonetsa anthu omwe akuwaganizira milandu yosiyanasiyana akumwa mowa koma ali m’chitokosi. Malingana ndi […]

The post A polisi awiri amangidwa ku Karonga pothandizira kulowesa mowa mu cell appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください