Anthu awiri ali mchitokosi cha polisi ku Lilongwe powaganizira kuti anali nawo m’gulu la anthu anayi omwe adabera munthu yemwe anakwera galimoto yawo ndalama yokwana 64 000 dollars (pafupifupi K111 million). Apolisi apezaponso K5 million pa ndalama yobedwayo komanso galimoto la mtundu wa Honda Fit ya ndalama pafupifupi K10 million, yomwe akuganizira kuti idagulidwa ndi […]
The post A polisi amanga anthu awiri pokuva ndalama pafupifupi K111 million kwa munthu yemwe anawapasa lift appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.