A Ngalande adasiya kutilabadira – adandaula anthu a kwa Kachenga

Anthu okhala m’dera la mfumu yaikulu Kachenga m’boma la Balaka ati ndi okhumudwa ndi phungu wa nyumba ya malamulo wa m’dera la kumpoto m’boma la Balaka a Tony Ngalande ati kaamba kakuti adasiya kuwalabadira mu ntchito za chitukuko. Poyankhulapo pakutha pa zokambilana  zomwe adakonza akuluakulu a komiti yoyendetsa ntchito za chitukuko mderari (Kachenga ADC), Mfumu […]

The post A Ngalande adasiya kutilabadira – adandaula anthu a kwa Kachenga appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください