Anthu okhala m’dera la mfumu yaikulu Kachenga m’boma la Balaka ati ndi okhumudwa ndi phungu wa nyumba ya malamulo wa m’dera la kumpoto m’boma la Balaka a Tony Ngalande ati kaamba kakuti adasiya kuwalabadira mu ntchito za chitukuko. Poyankhulapo pakutha pa zokambilana zomwe adakonza akuluakulu a komiti yoyendetsa ntchito za chitukuko mderari (Kachenga ADC), Mfumu […]
The post A Ngalande adasiya kutilabadira – adandaula anthu a kwa Kachenga appeared first on Malawi24.