Wolemba: Sopani Ng’ambi Wachiwiri kwa mfumu ya mzinda wa Mzuzu, a Tony Gradwell Mwenitete, wapempha zipani za ndale m’dziko muno kuti zizigwira bwino ntchito ndi achinyamata powaphunzitsa makhalidwe oyenera omwe angawathandizire kukhala nzika zodalirika. Iwo adanena izi pa mwambo womwe achinyamata a chipani cha Malawi Congress Party ochokera m’mzinda wa Mzuzu amapereka katundu osiyanasiyana monga […]
The post A ndale awapempha kuti azigwira bwino ntchito ndi achinyamata appeared first on Malawi 24.