Yemwe adali wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha DPP kummwera, a Kondwani Nankhumwa, watengera chipani cha DPP ku bwalo la milandu, kutsutsana ndi kuchotsedwa kwawo m’chipanichi. Malinga ndi owayimira a Nankhumwa, a Wapona Kita, a Nankhumwa adachotsedwa m’chipanichi mosatsata malamulo. A Kita ati nkhaniyi idzamvedwa ndi oweruza mlandu ku bwalo lalikulu la milandu a […]
The post A Nankhumwa abweleranso ku court: Ati sanakondwe ndi mmene anawachosera mu chani cha DPP appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.