Mtsogoleri wakale wa dziko lino yemwenso ndi Mtsogoleri wa Chipani cha Democratic Progressive Party-DPP, His Excellency Professor Arthur Peter Mutharika, lero chakusanaku anakachezera asilamu pa Mzikiti wa Mangochi Main Mosque ntown ya Mangochi. Mwachizowezi, a Mutharika anachezera komanso kuwalimbikisa abale ndi alongo achisilamu amene padakali pano ali mu nyenyo Ramadan. Iwo ananena kuti nyenyo ya […]
The post A Mutharika achezera Asilamu pa Mzikiti wa Mangochi main, agawa zakudya zambiri appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.