A Malawi oposa 200 akupita ku Israel kukagobola

Ndege yomwe ikuyembekezeka kunyamula a Malawi oposa 200 omwe boma likuti lawapezera ntchito m’dziko la Israel, yafika kale m’dziko muno ndipo anthuwa anyamuka pakati pausiku lero. Ndege yonyamula anthuwa yomwe ndiya aRKIA Airbus a321-251NX, inatela pa bwalo la ndege la Kamuzu ku Lilongwe momwe nthawi imati 1:42 lero lachisanu pa 24 November, 2023 ndipo akuluakulu […]

The post A Malawi oposa 200 akupita ku Israel kukagobola appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください