A Malawi odana ndi Katangale 1, a Chakwera ndi Zamba 0

…Khoti labwenzeretsa Mayi Chizuma Tsiku lofa nyani mtengo ulionse umatelera. Boma la a Lazarus Chakwera lakumana nazo ku bwalo pamene oweruza ayimitsa kaye chiganizo choti awapumitse pa ntchito. Bungwe la maloya mu dziko lino, Malawi Law Society, latenga chiletso pa chiganizo chofuna kuimitsa ntchito Mayi Martha Chizuma. Malinga ndi zikalata za ku bwalo lamilandu lalikulu, […]

The post A Malawi odana ndi Katangale 1, a Chakwera ndi Zamba 0 appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください