Pamene dziko la Malawi likupitilira kukumana ndi mavuto osiyanasiyana pankhani yokhudza zachuma, katswiri pa nkhani ya zachuma a Betchani Tchereni wawuza a Malawi kuti ayembekezere kuti pali kuthekera koti mitengo ya zinthu pa msika ipitilira kukwera. Malingana ndi a Tchereni, izi zikuyenera kuchitika chonchi pamene ndalama ya dziko lino sinakhazikikebe pa msika. Iwo anapitilizanso kunena […]
The post A Malawi ayembekezere kupitilira kukwera kwa mitengo ya zinthu, watero Katswiri pa zachuma appeared first on Malawi 24.