A Malawi akunyinyilika Wode Maya atatchula mbewa kuti soseji

Inde mlendo Wode Maya wadza nkalumo kakuthwa, komatu wadzetsa kung’ung’udza m’masamba anchezo pa mpanje pano kaamba koti waliuza dziko la pansi kuti ku Malawi kuno mbewa zija ndi makoswe komanso akuti ‘makoswewo’ timawatchula kuti soseji ya mu Africa. Wode Maya yemwe dzina in a lake lenileni ndi Berthold Kobby Winkler Ackon ochokera m’dziko la Ghana, […]

The post A Malawi akunyinyilika Wode Maya atatchula mbewa kuti soseji appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください