A Malawi aikila kumbuyo ganizo lopanga lamulo lomwe lidziletsa nkhalamba kuima pa chisankho

A Malawi ambiri omwe tayankhula nawo aikila kumbuyo ganizo lomwe anthu wena akhala akunena kuti pakhale lamulo lomwe cholinga chake ndi kuonenetsa kuti pakhale  malire a zaka zomwe munthu akuyenera akhale nazo kuti aime pa masankho a utsogoleri wa dziko lino.   Izi zikuchitika ngakhale zipani dzotsitsa boma zakhala zikukana ganizoli potengera kutimtsogoleri wawo kuchipani […]

The post A Malawi aikila kumbuyo ganizo lopanga lamulo lomwe lidziletsa nkhalamba kuima pa chisankho appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください