A Malawi adzudzula Chakwera pa nkhani ya ntchito zoposa 900,000

Anthu m’dziko muno akudzudzula mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera pabodza lankunkhuniza lomwe wayankhula kuti boma la Tonse lapanga ntchito zoposa 900,000. Potsekulira nyumba ya malamulo Lachinayi mumzinda wa Lilongwe a Chakwera anatutumutsa anthu pomwe anati boma lawo lakwanitsa kupanga ntchito zokwana 997,423 mumzaka ziwiri. A Chakwera omwe nthawi yokopa anthu kuti awavotele analonjeza […]

The post A Malawi adzudzula Chakwera pa nkhani ya ntchito zoposa 900,000 appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です