A Kalindo ati akachita nawo zionetsero

Pamene oyankhula pa fesibuku Joshua Chisa Mbele yemweso ndi mmodzi mwa akuluakulu abungwe la Citizens Against Impunity and Corruption waitanitsa zionetsero sabata yamawa, Bon Kalindo yemwe mmbuyomu analankhula kuti ‘a Malawi siowafela’ wati akachita nawo zionetserozo. Kumayambiliro kwa sabata ino, Chisa Mbele walengeza kuti Lachinayi sabata yamawa pa 27 October, kukhala zionetsero za dziko lonse […]

The post A Kalindo ati akachita nawo zionetsero appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください