A Bon Kalindo akhala akusungidwabe mchitokosi cha apolisi uku akudikira chigamulo kuchokera kwa woweruza milandu a Muhammad Maxwell Chande lachisanu likudzali pa 15 December. A Kalindo anawanjata sabata latha m’boma la Zomba powaganizira kuti iwo anayambitsa chisokonezo komanso ziwawa pa zionetsero zomwe zidachitika kumapeto a mwezi watha m’boma la Zomba. A Kalindo akhala akutsogolera zionetsero […]
The post A Kalindo akhalabe mkambolimboli uku akudikira chigamulo appeared first on Malawi 24.