A Jeffrey akubweretsa chisokonezo ku DPP, watero Msaka

Wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha Democratic Progressive Party (DPP) wa chigawo cha ku m’mawa a Bright Msaka wati zomwe aanchita mlembi wachipanichi  Grezeldar  Jeffrey poitanitsa msonkhano wa komiti yaikulu yoyendetsa DPP opanda chilolezo cha pulezidenti wachipanichi ndikupeputsa mtsogoleri was DPP a Peter Mutharika komanso kubweretsa chisokonezo. A Msaka anena izi pa msonkhano omwe unachitika […]

The post A Jeffrey akubweretsa chisokonezo ku DPP, watero Msaka appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください