Poyendera nyumba za a chitetezo zomwe akuzimanga ku Mitole m’boma la Chikwawa, mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wati Nyumba zomangidwa zikuyenera kutsata ndondomeko zabwino zomangira kuti zizikhala zolozeka. Polankhula m’mau awo m’mawa wa lero, a Chakwera ayamikila ntchito yomanga nyumba za a polisi zokwana makumi atatu (30) yomwe ili mkati m’bomali ndipo ati ntchito […]
The post A Chakwera ati zomanga zitsate ma sitandadi appeared first on Malawi 24.