A Chakwera ati Chitani Ulimi musadzimve u Big

Mtsogoleri wa dziko lino, Lazarus Chakwera, walimbikitsa a Malawi onse kuti asangodalira ntchito za mu ofesi koma adzichitanso ulimi komanso kusatsa malonda a zolima ponena kuti dziko la Malawi liri ndi chuma chochuluka mu ulimi. Potsekulira sabata ya chionetselo cha za ulimi ku Bingu International Convention Centre (BICC) mu Mzinda wa Lilongwe, a Chakwera ati […]

The post A Chakwera ati Chitani Ulimi musadzimve u Big appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください