A Chakwera amazitamandira ndi ntchito zomwe zinayambika nthawi ya DPP, atero a Navicha

Mtsogoleri wa chipani cha DPP ku Nyumba ya Malamulo, Mary Navicha, wadzudzula boma la Tonse kamba kodzitamandira pa ntchito zachitukuko zomwe zidayambika panthawi yomwe DPP inali m’boma. Izi zadza pomwe nduna zosiyanasiyana za mbali ya boma zimafotokoza zina mwa ntchito zachitukuko zomwe zikuchitika mdziko muno m’maboma osiyanasiyana. Polankhula , Mary Navicha yemwe adasankhidwa kukhala mtsogoleri […]

The post A Chakwera amazitamandira ndi ntchito zomwe zinayambika nthawi ya DPP, atero a Navicha appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください