Patangotha masiku ochepa chibwelereni kuchokera ku Amerika, mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera mawa anyamuka kupita ku Mozambique. A Chakwera anyamuka ku Mozambique mawa ndipo akabwerako tsiku lomwelo. Malingana ndi nduna ya zofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu, a Chakwera ku Mozambique akakumana ndi mtsogoleri wa dzikolo a Felipe Nyusi komanso mtsogoleri wa dziko la […]
The post A Chakwera akupita ku Mozambique mawa appeared first on Malawi 24.