A Chakwera akulowela nawo achinyamata ku thengo – watelo kafukufuku

Zangolunjikana ndi sabata yomwe boma laganiza kuchotsa milandu yokhudza za Katangale  ya wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko la Malawi a Saulos Chilima ngakhale bungwe lothana ndi Katangale la Anti- Corruption Bureau (ACB) linati lili ndi ma umboni okwanila a zakatangale zomwe a Chilima adachita. A chilima amayimbidwa mulandu woti adalandira chiphuphu kwa wakatangale ochita malonda Zuneth […]

The post A Chakwera akulowela nawo achinyamata ku thengo – watelo kafukufuku appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください