A Chakaka Nyirenda atule pansi udindo – yatero CDEDI

Bungwe lolimbikitsa chilungamo komanso kuunikira momwe Boma likuyendera la Centre for Democracy and Economic Initiatives (CDEDI) lati mlangizi wa boma nkhani za malamulo (Attorney General) Thabo Chakaka Nyirenda atule pansi udindo ngati sapereka umboni pa za ndalama yokwana K750 Million ya ndondomeko ya zipangizo za ulimi zotsika mtengo (AIP) yomwe inalipilidwa kwa ochita malonda ogulitsa […]

The post A Chakaka Nyirenda atule pansi udindo – yatero CDEDI appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください