Mmodzi mwa anthu omwe anachotsedwa mchipani cha Malawi Congress Party-MCP Alex Major wati zomwe apanga achipanichi podzudzula DPP pochotsa anthu ena ‘ndizogwetsa ulesi’. Major anachotsedwa mchipani cha MCP mu 2022 ponena kuti samalemekeza mfundo zamtsogoleri wawo Lazarus Chakwera. Poyankhula ndi Nyasatimes, Major wati ndizoseketsa kwambiri pakalata yomwe atulutsa a MCP kamba koti iyeyo anachotsedwa atangolembeledwa […]
The post A Alex Major, omwe anachosedwa mu MCP, adzudzula MCP podzudzula DPP appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.