Zina ukamva kamba anga mwala. apolisi ku Zomba akusakasaka mbava yomwe yaba mfuti, zipolopolo khumi komaso ma foni a m ’manja awiri mu ofesi ya apolisi. Malipoti akusonyeza kuti nkhaniyi yomwe yadulitsa mitu yazizwa, yachitika cha mma 5 kololoko m’mawa wa lolemba pa 14 February, 2022 ku ofesi ya polisi ya Zomba. Zikuveka kuti mbava […]
The post Mbava yaba mfuti, zipolopolo ku polisi appeared first on Malawi 24.