A Mpinganjira atuluka kundende pa belo

Mpondamatiki Thom Mpinganjira tsopano akupuma mpweya wabwino bwalo la milandu la apilu litalamula kuti atuluke ku ndende pa belo. A Mpinganjira analamulidwa kukakhala ku ndende kwa zaka zisanu ndi zinayi (9) kaamba kowaganizira kuti ankafuna kupeleka ziphuphu kwa oweruza milandu omwe amayendetsa mlandu wa chisankho chaka cha 2019. Koma ataseweza jele kwa miyezi itatu yokha, […]

The post A Mpinganjira atuluka kundende pa belo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です