Kabambe watsimikizila anthu ku Mchinji za ubwino oyika anthu odziwa ntchito m’malo mwake

Mtsogoleli wa chipani cha UTM a Dalitso Kabambe wauza anthu m’boma la Mchinji kuganizila zoika m’maudindo atsogolela oyenelela kugwila ntchito zokweza chuma cha dziko lino pomwe chisankho chikuyandikila. Pa misokhano yawo yokopa anthu yomwe anali nayo m’bomali a Kabambe atsindika kuti ntchito yoyendetsa dziko sifuna munthu ophunzilila koma yemwe ali ndi kuthekela kale. “Dzulo, tinakambirana […]

The post Kabambe watsimikizila anthu ku Mchinji za ubwino oyika anthu odziwa ntchito m’malo mwake appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください