Kuchotsa ndale za zipani kungathandize kusintha dziko lino – Tobias

Yemwe akufuna kudzayimira nawo pa udindo wa mtsogoleri wa dziko, Milward Tobias, wati kuthetsa ndalenza zipani ndi njira imodzi yomwe ingathandize potukula dziko lino. Tobias wati ndi chifukwa chake iye akufuna kudzayimira nawo pa mpandowu posayimira chipani chilichonse. “Ine Milward Tobias ndidzaima pa udindo wa mtsogoleri wa dziko chisankho cha pa 16 September chaka chino. […]

The post Kuchotsa ndale za zipani kungathandize kusintha dziko lino – Tobias appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください