Kampani yopanga magetsi mdziko muno ya Electricity Generation Company (EGENCO) yati siikudziwa kuti vuto lakuzimazima kwa magetsi, lomwe layamba kaamba ka mvula yamphamvu, litha liti. Nkhaniyi ikutsatira kuzimitsidwa kwa makina m ’malo ena opangira magetsi lolemba pa 24 January kaamba ka mvula ya mphamvu yomwe mmadera ambiri mdziko muno zomwe zapangitsa kuti mitsinje yochuluka kuphatikizapo […]
The post Sitikudziwa kuti musiya kukhala mu mdima liti – yatelo EGENCO appeared first on Malawi 24.