Promise Kamwendo abwerere ku Dedza Dynamos, yatero FAM

Bungwe loyendetsa mpira la FAM lagamula kuti osewera kutsogolo, Promise Kamwendo abwelere ku team yake ya Dedza Dynamos kamba kakuti mgwirizano omwe osewerayu adasainila ndi team ya Mighty Mukuru Wanderers ngosavomerezeka. Bungweli lalamuranso osewerayu kubwenza 6 million kwacha yomwe adapochera, yomwe pachingelezi amati ‘signing on fee’ ku team ya Wanderers. FAM yatinso team ya Dedza […]

The post Promise Kamwendo abwerere ku Dedza Dynamos, yatero FAM appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください