Mamembala achipani cha UTM omwe tinakwanitsa kucheza nawo adandaula ndi zochita za mlembi wamkulu a Patricia Kaliati kuti akuchita zodelera mtsogoleri wachipani chawo, a Dr Michael Biswick Usi. Malingana ndi mamembala amenewa omwe sitiwatchula mayina, a Kaliati akhala akupanga ziganizo zochuluka pamodzi ndi anzawo ena mchipanichi zomwe sadafunse maganizo kwa mtsogoleri wachipanichi a Dr Usi. […]
The post A Kaliati awadzudzula kamba kobweretsa mpungwepungwe mchipani cha UTM appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.