Engineer Mumba walumira mano ndipo wanenetsa kuti: “Ndikuyima ndipo ndikapambana!”

Engineer Vitumbiko Mumba walumira mano ndipo wanenetsa kuti iyeyo sanaluzepo zisankho choncho pa 8 August pano akayima ndikukatenga mpando wa wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha MCP. Iyeyu, poyankhula ndi kanema wa Times usiku wathawu, watemesa nkhwangwa pa mwala kuti palibe chikuwaopsa kuti chingawagwetse osatenga udindowu. “Chipani cha MCP chikufunika wachiwiri kwa mtsogoleri  wachinyamata yemwe […]

The post Engineer Mumba walumira mano ndipo wanenetsa kuti: “Ndikuyima ndipo ndikapambana!” appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください