Uladi Mussa wapempha nthumwi za MCP kuti ‘chonde, chonde, kavomerezeni Chakwera azayimilenso’

Mkhala kale pa ndale, Uladi Mussa, wapempha nthumwi ku msonkhano waukulu wa chipani cha MCP kuti zikavomereze dzina la mtsogoleri wadziko lino a Lazarus Chakwera kuti adzaimilenso chipanichi pa chisankho cha chaka chamawa. Polankhula ndi olemba nkhani mumzinda wa Lilongwe, a Mussa ati utsogoleri wa a Chakwera waonetselatu kuti ndi umene ungatulule dziko lino.   […]

The post Uladi Mussa wapempha nthumwi za MCP kuti ‘chonde, chonde, kavomerezeni Chakwera azayimilenso’ appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください