Wapsa waku Israel: Achinyamata 500 anyamuka mu mwezi wa August

Achinyamata okwana 500 ndi omwe akuyembekezeka kunyamuka mwezi wa mawa kupita kukagwira tchito mdziko la Israel. Mmodzi mwa akuluakulu ku unduna wa za ntchito a Paul Kalilombe wauza komiti ya Public Accounts ku nyumba ya malamulo kuti izi zili chonchi molingana ndi zomwe maiko a Malawi ndi Israel adakambirana posachedwapa. Iwo ati boma lapatsidwa mwayi oti […]

The post Wapsa waku Israel: Achinyamata 500 anyamuka mu mwezi wa August appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください