Pali kuthekera kwakukulu kuti anthu ena omwe angolowa kumene chipani cha Malawi Congress (MCP) sakapikisana nawo ku msonkhano waukulu wachipani-chi pamene komiti yomwe ikuyendetsa msonkhanowu ikuwunikira zikalata za opikisana. Anthu omwe awonetsa chidwi kukapikisana nawo pa maudindo osiyana-siyana apereka zikalata zawo, koma komiti ikuwunika pofuna kupeza omwe ali ovomerezeka. Nkhalapampando wakomiti yomwe ikuyendetsa zokonzekera za […]
The post Ena aletsedwa kuyima ku konveshoni ya MCP appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.