Mtsogoleri wa dziko lino Dr. Lazarus McCarthy Chakwera wati ndiwowawidza mtima komanso kukhudzika kwambiri ndi umphawi womwe aMalawi akumudzi komanso achinyamata amakumana nawo. Chakwera wati ichi ndi chifukwa chake kuyambira pamene adasankhidwa kukhala mtsogoleri wa dziko lino, boma lake lidakhazikitsa masomphenya a Malawi 2063, omwe cholinga chake ndikukhazikitsa njira zochulukitsira chuma cha aMalawi. Mtsogoleriyu wanena […]
The post Ndimawawidwa mtima ndi umphawi wa akumudzi ndi achinyamata – Chakwera appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.