Chakwera, mavenda achigawo chakumvuma agwirizana zogwira ntchito limodzi potukula Malawi

Mtsogoleri wa dziko la Dr. Lazarus McCarthy Chakwera Lachinayi madzulo adakumana ndi kukambirana ndi ochita malonda ochokera ku chigawo chakumvuma cha dziko pofuna kulimbikitsa ubale ndi umodzi potukula Malawi. Mkumanowo udachitikira ku nyumba ya boma ya Chikoko Bay State Lodge ndipo udayitanitsidwa ndi cholinga chowapatsa mavendawa mwayi wokumana ndi mtsogoleri wa dziko. Polankhula pa mkumanowo, […]

The post Chakwera, mavenda achigawo chakumvuma agwirizana zogwira ntchito limodzi potukula Malawi appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください